Genesis 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chilichonse chokhala ndi mpweya wa moyo* m’mphuno mwake, kutanthauza zonse zimene zinali pamtunda, zinafa.+ Numeri 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inu Yehova, Mulungu wa miyoyo ya zamoyo+ zamitundu yonse,+ sankhani munthu woti aziyang’anira khamuli.+ Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+
22 Chilichonse chokhala ndi mpweya wa moyo* m’mphuno mwake, kutanthauza zonse zimene zinali pamtunda, zinafa.+
16 “Inu Yehova, Mulungu wa miyoyo ya zamoyo+ zamitundu yonse,+ sankhani munthu woti aziyang’anira khamuli.+
29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+