Numeri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+ Yobu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye amene moyo+ wa aliyense uli m’dzanja lake,Ndiponso mzimu wa anthu onse.+
22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+