Genesis 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+ 2 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide atangoona mngelo amene anali kupha anthuyo anauza Yehova kuti: “Tsopano amene ndachimwa ndine, ndipo ine ndi amene ndachita cholakwa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Dzanja lanu likhale pa ine+ chonde ndi panyumba ya bambo anga.”
23 Ndiyeno Abulahamu anamuyandikira n’kuyamba kumufunsa kuti: “Kodi zoona mungawononge olungama pamodzi ndi oipa?+
17 Ndiyeno Davide atangoona mngelo amene anali kupha anthuyo anauza Yehova kuti: “Tsopano amene ndachimwa ndine, ndipo ine ndi amene ndachita cholakwa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Dzanja lanu likhale pa ine+ chonde ndi panyumba ya bambo anga.”