Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma Abimeleki anali asanagone naye Sarayo.+ Chotero iye anati: “Yehova, kodi mudzapha mtundu wosalakwa?+

  • Numeri 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anthuwo atamva zimenezi anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, n’kunena kuti: “Chonde Mulungu, inu Mulungu amene amapereka moyo kwa zamoyo zonse,+ kodi kuchimwa kwa munthu mmodzi yekha n’kumene mungapsere mtima khamu lonseli?”+

  • Yobu 34:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,

      Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+

      Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+

  • Yeremiya 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose+ ndi Samueli+ akanaima pamaso panga, anthu awa sindikanawakomera mtima.+ Ndikanawapitikitsa pamaso panga kuti achoke.+

  • Mateyu 13:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pa mapeto a nthawi* ino: Angelo adzapita n’kukachotsa oipa+ pakati pa olungama+

  • Aroma 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Komabe, ngati kulungama kwa Mulungu+ kukuonekera chifukwa cha kusalungama kwathu, ndiye tinene kuti chiyani? Kodi tingati Mulungu ndi wosalungama+ poonetsa mkwiyo wake? (Ndikulankhula mmene anthu+ amalankhulira.)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena