Yobu 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba? Miyambo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wolemera ndiponso munthu wosauka n’chimodzimodzi.+ Amene anapanga onsewa ndi Yehova.+
15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba?