Yobu 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba? Yobu 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+ Machitidwe 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+
15 Kodi amene anandipanga m’mimba si amene anapanganso iyeyo?+Kodi si mmodzi yemweyo amene anatipanga tonsefe m’mimba?
19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+
26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+