2 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+ Yeremiya 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndidzakuthamangitsani, kukuchotsani pamaso panga,+ ngati mmene ndinathamangitsira abale anu onse, mbadwa zonse za Efuraimu.’+
20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+
15 Ine ndidzakuthamangitsani, kukuchotsani pamaso panga,+ ngati mmene ndinathamangitsira abale anu onse, mbadwa zonse za Efuraimu.’+