2 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale? Yeremiya 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu adzawatcha, ‘siliva wokanidwa,’+ pakuti Yehova wawakana.”+
7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale?