Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+ Yakobo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho linakwaniritsidwa lemba limene limati, “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova,* ndipo anaonedwa ngati wolungama,”+ choncho anatchedwa “bwenzi la Yehova.”+
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+
23 Choncho linakwaniritsidwa lemba limene limati, “Abulahamu anakhulupirira mwa Yehova,* ndipo anaonedwa ngati wolungama,”+ choncho anatchedwa “bwenzi la Yehova.”+