Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Levitiko 25:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo.
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo.