Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Levitiko 25:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 “‘Pakuti kwa ine ana a Isiraeli ndi akapolo. Ndi akapolo anga+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
55 “‘Pakuti kwa ine ana a Isiraeli ndi akapolo. Ndi akapolo anga+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+