Deuteronomo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Onani, Yehova Mulungu wanu wakusiyirani dzikoli.+ Pitani, litengeni kuti likhale lanu, monga momwe Yehova Mulungu wa makolo anu anakuuzirani.+ Musaope kapena kuchita mantha.’+ Yoswa 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+
21 Onani, Yehova Mulungu wanu wakusiyirani dzikoli.+ Pitani, litengeni kuti likhale lanu, monga momwe Yehova Mulungu wa makolo anu anakuuzirani.+ Musaope kapena kuchita mantha.’+
9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+