Deuteronomo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+ Yoswa 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo. Nyamuka, upite kudziko la Ai. Taona, mfumu ya Ai ndaipereka m’manja mwako limodzi ndi anthu ake, mzinda wake, ndi dziko lake.+
8 Yehova ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye adzapitiriza kuyenda nanu.+ Sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono. Choncho musaope kapena kuchita mantha.”+
8 Tsopano Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo. Nyamuka, upite kudziko la Ai. Taona, mfumu ya Ai ndaipereka m’manja mwako limodzi ndi anthu ake, mzinda wake, ndi dziko lake.+