Salimo 119:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mwatilamula kuti tisunge+Malamulo anu mosamala.+ Miyambo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wosunga lamulo akusunga moyo wake.+ Wosasamala za njira zake adzaphedwa.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+