1 Mafumu 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso kuti m’nyumbamo ndisankhemo malo oika Likasa, lomwe muli pangano+ la Yehova limene anapangana ndi makolo athu pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.” Salimo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+ Agalatiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira,+ pakuti azimayi amenewa akuimira mapangano awiri.+ Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndiye Hagara uja.
21 Komanso kuti m’nyumbamo ndisankhemo malo oika Likasa, lomwe muli pangano+ la Yehova limene anapangana ndi makolo athu pamene anali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo.”
10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+
24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira,+ pakuti azimayi amenewa akuimira mapangano awiri.+ Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndiye Hagara uja.