2 Mbiri 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale? Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+
7 Kodi inuyo Mulungu wathu+ si paja munathamangitsa anthu amene anali kukhala m’dziko lino pamaso pa anthu anu Aisiraeli,+ n’kulipereka+ kwa mbewu ya Abulahamu yemwe anali kukukondani,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale?
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+