Mateyu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi. Aheberi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti iye sakuthandiza angelo ngakhale pang’ono, koma akuthandiza mbewu ya Abulahamu.+
9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.