Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+