2 Mbiri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno munthu winawake wa Mulungu woona+ anapita kwa Amaziya n’kumuuza kuti: “Inu mfumu, musalole kuti gulu lankhondo la Isiraeli lipite nanu limodzi, chifukwa Yehova sali ndi Aisiraeli,+ kutanthauza ana onse a Efuraimu. Salimo 78:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Iye anakana hema wa Yosefe,+Ndipo sanasankhe fuko la Efuraimu.+
7 Ndiyeno munthu winawake wa Mulungu woona+ anapita kwa Amaziya n’kumuuza kuti: “Inu mfumu, musalole kuti gulu lankhondo la Isiraeli lipite nanu limodzi, chifukwa Yehova sali ndi Aisiraeli,+ kutanthauza ana onse a Efuraimu.