2 Mafumu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mkwiyo wa Yehova+ unawayakira Aisiraeli, moti nthawi zonse ankawapereka m’manja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli.
3 Choncho mkwiyo wa Yehova+ unawayakira Aisiraeli, moti nthawi zonse ankawapereka m’manja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli.