1 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+ Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+