Salimo 106:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+
23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+