Ekisodo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu? Deuteronomo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu?
19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+