Ekisodo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu? Ekisodo 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo, Yehova anayamba kumva chisoni chifukwa cha tsoka limene ananena kuti agwetsera anthu ake.+ Deuteronomo 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ine ndinakhala m’phirimo masiku ofanana ndi oyamba aja, masiku 40, usana ndi usiku,+ ndipo Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ Yehova sanafune kukuwonongani.+ Salimo 106:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+
11 Pamenepo Mose anakhazika pansi mtima wa Yehova Mulungu wake.+ Iye anati: “N’chifukwa chiyani, inu Yehova, mukufuna kuti mkwiyo wanu+ uyakire anthu anu, amene munawatulutsa m’dziko la Iguputo mwa mphamvu zazikulu ndiponso ndi dzanja lamphamvu?
14 Pamenepo, Yehova anayamba kumva chisoni chifukwa cha tsoka limene ananena kuti agwetsera anthu ake.+
10 Ndipo ine ndinakhala m’phirimo masiku ofanana ndi oyamba aja, masiku 40, usana ndi usiku,+ ndipo Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ Yehova sanafune kukuwonongani.+
23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+