Deuteronomo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zitatero ndinadzigwetsa pansi pamaso pa Yehova masiku 40, usana ndi usiku, ngati mmene ndinachitira poyamba. Sindinadye mkate kapena kumwa madzi+ chifukwa cha machimo anu onse amene munachita ndi kukhumudwitsa Yehova, mwa kuchita zinthu zoipa pamaso pake.+ Salimo 106:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+
18 Zitatero ndinadzigwetsa pansi pamaso pa Yehova masiku 40, usana ndi usiku, ngati mmene ndinachitira poyamba. Sindinadye mkate kapena kumwa madzi+ chifukwa cha machimo anu onse amene munachita ndi kukhumudwitsa Yehova, mwa kuchita zinthu zoipa pamaso pake.+
23 Iye anangotsala pang’ono kulamula kuti awawononge,+Koma Mose wosankhidwa wake,Anaima pamalo ogumuka pamaso pa Mulungu,+Ndi kubweza mkwiyo wake kuti usawawononge.+