Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+ Hoseya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto.+ Sindidzawononganso Efuraimu+ pakuti ndine Mulungu+ osati munthu. Ndine Woyera pakati panu+ ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya. Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+
45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+
9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto.+ Sindidzawononganso Efuraimu+ pakuti ndine Mulungu+ osati munthu. Ndine Woyera pakati panu+ ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya.
13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+