Deuteronomo 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndinakhala mʼphirimo kwa masiku 40, masana ndi usiku,+ ngati mmene ndinachitira poyamba paja. Pa nthawi imeneyinso Yehova anandimvetsera.+ Yehova sankafuna kukuwonongani.
10 Ine ndinakhala mʼphirimo kwa masiku 40, masana ndi usiku,+ ngati mmene ndinachitira poyamba paja. Pa nthawi imeneyinso Yehova anandimvetsera.+ Yehova sankafuna kukuwonongani.