Deuteronomo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+
19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+