-
1 Mbiri 21:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako Davide anauza Mulungu woona kuti: “Kodi si ine amene ndinalamula kuti awerenge anthu? Ndipo kodi si ine ndachimwa ndi kuchitadi cholakwa?+ Nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Chonde Yehova Mulungu wanga, dzanja lanu likhale pa ine ndi panyumba ya bambo anga, koma mliriwu usakhale pa anthu anu.”+
-