2 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide atangoona mngelo amene anali kupha anthuyo anauza Yehova kuti: “Tsopano amene ndachimwa ndine, ndipo ine ndi amene ndachita cholakwa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Dzanja lanu likhale pa ine+ chonde ndi panyumba ya bambo anga.” Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
17 Ndiyeno Davide atangoona mngelo amene anali kupha anthuyo anauza Yehova kuti: “Tsopano amene ndachimwa ndine, ndipo ine ndi amene ndachita cholakwa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Dzanja lanu likhale pa ine+ chonde ndi panyumba ya bambo anga.”
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+