Luka 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+ Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+
29 (Pamenepo anthu onse ndi okhometsa msonkho omwe atamva zimenezi, analengeza kuti Mulungu ndi wolungama,+ popeza iwo anali atabatizidwa ndi ubatizo wa Yohane.+
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+