Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+

      Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+

      Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+

      Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”

  • 2 Mafumu 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ukaphe anthu a m’nyumba ya mbuye wako Ahabu, kuti ine ndibwezere+ magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anapha.+

  • Salimo 79:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+

      Pamene mukubwezera anthu a mitundu inawo chifukwa cha magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa,+

      Ife tidzaone ndi maso athu.+

  • Chivumbulutso 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

  • Chivumbulutso 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mwa iye munapezeka magazi+ a aneneri,+ a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena