Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+

  • 1 Mafumu 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.”

  • 1 Mafumu 21:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, nthawi yomweyo anauza Ahabu kuti: “Nyamukani, katengeni munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, popeza Naboti salinso moyo koma wafa.”

  • 1 Mafumu 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena