Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+