1 Mafumu 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ahabu mwana wa Omuri anachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+
30 Ahabu mwana wa Omuri anachita zoipa kwambiri pamaso pa Yehova kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+