1 Mafumu 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Omuri anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anachita zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+ 1 Mafumu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo. 2 Mafumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+
25 Omuri anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anachita zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+
25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.
2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+