Yobu 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti maso ake amayang’anitsitsa njira za munthu,+Ndipo amaona mayendedwe ake onse.