1 Mafumu 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Komanso, ngati kuti kuyenda m’machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati inali nkhani yaing’ono,+ Ahabu anakwatira+ Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kukatumikira Baala+ ndi kum’gwadira.
31 Komanso, ngati kuti kuyenda m’machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati inali nkhani yaing’ono,+ Ahabu anakwatira+ Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kukatumikira Baala+ ndi kum’gwadira.