Deuteronomo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+ Yoswa 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma mukatembenuka+ n’kumamatira zotsala za anthu awa a mitundu ina,+ amene atsala pakati panuwa, kumakwatirana nawo,+ n’kumakhala pakati pawo, iwonso n’kumakhala pakati panu,
3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+
12 “Koma mukatembenuka+ n’kumamatira zotsala za anthu awa a mitundu ina,+ amene atsala pakati panuwa, kumakwatirana nawo,+ n’kumakhala pakati pawo, iwonso n’kumakhala pakati panu,