Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+

  • Deuteronomo 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+

  • Oweruza 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aisiraeli anatenga ana aakazi a Akanani kukhala akazi awo,+ ndipo ana awo aakazi anawapereka kwa ana aamuna a Akanani,+ moti Aisiraeli anayamba kutumikira milungu ya Akanani.+

  • 1 Mafumu 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.

  • Ezara 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo alola ena mwa ana aakazi a mitundu inayo kuti akhale akazi awo ndi akazi a ana awo aamuna,+ ndipo iwo omwe ndi mtundu wopatulika,+ asakanikirana+ ndi anthu a mitundu ina. Akalonga ndi atsogoleri ndiwo ali patsogolo+ pa kusakhulupirika kumeneku.”

  • Nehemiya 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Komanso ndinaona kuti Ayuda ena anali atakwatira+ akazi achiasidodi,+ achiamoni ndi achimowabu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena