Nehemiya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho atangomva chilamulocho,+ anayamba kupatula+ khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana kuwachotsa pakati pa Isiraeli. 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
3 Choncho atangomva chilamulocho,+ anayamba kupatula+ khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana kuwachotsa pakati pa Isiraeli.
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+