Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 119:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzasinkhasinkha malamulo anu,+Ndipo ndidzalabadira njira zanu.+ Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+