Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+

      Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+

  • Salimo 111:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chiweruzo.+

      נ [Nun]

      Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+

  • Salimo 119:93
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  93 Sindidzaiwala malamulo anu mpaka kalekale,+

      Chifukwa mwandisungabe wamoyo kudzera m’malamulo amenewo.+

  • Salimo 119:100
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 100 Ndimachita zinthu mozindikira kuposa anthu achikulire,+

      Chifukwa ndimasunga malamulo anu.+

  • Salimo 119:173
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 173 Dzanja lanu lindithandize,+

      Chifukwa ndasankha malamulo anu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena