Salimo 103:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+ Salimo 119:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mwatilamula kuti tisunge+Malamulo anu mosamala.+ Salimo 119:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndi zimenetu zandichitikira ine,Chifukwa ndimatsatira malamulo anu.+
18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+