Salimo 119:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndasunga mosamala mawu anu mumtima mwanga,+Kuti ndisakuchimwireni.+ Miyambo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+