Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo. Salimo 37:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chilamulo cha Mulungu wake chili mumtima mwake.+Poyenda mapazi ake sadzaterereka.+
13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.