Salimo 112:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+ Salimo 119:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndisanagwe m’masautso ndinali kuchimwa mosadziwa,+Koma tsopano ndimasunga mawu anu.+ Luka 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mariya anasunga mawu onsewa ndi kuganizira tanthauzo la zimenezi mumtima mwake.+ Luka 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+ Aroma 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+
112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+
51 Pamenepo ananyamuka nawo limodzi kubwerera ku Nazareti, ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+
17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+