Salimo 112:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Tamandani Ya!*+ א [Aleph] Wosangalala ndi munthu amene amaopa Yehova,+ב [Beth]Amene amasangalala kwambiri ndi malamulo ake.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 112:1 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, ptsa. 25-267/15/2000, tsa. 512/1/1987, tsa. 11
112 Tamandani Ya!*+ א [Aleph] Wosangalala ndi munthu amene amaopa Yehova,+ב [Beth]Amene amasangalala kwambiri ndi malamulo ake.+