Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+ Salimo 115:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu oopa Yehova, khulupirirani Yehova.+Iye ndiye thandizo lanu ndi chishango chanu.+ Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+
10 Chiyambi cha nzeru ndicho kuopa Yehova.+ ש [Sin]Onse otsatira malamulo a Mulungu ndi ozindikira.+ ת [Taw]Iye ayenera kutamandidwa mpaka muyaya.+