Miyambo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wosonyeza kuzindikira pa zinthu adzapeza zabwino,+ ndipo wodala ndi munthu amene amakhulupirira Yehova.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
20 Munthu wosonyeza kuzindikira pa zinthu adzapeza zabwino,+ ndipo wodala ndi munthu amene amakhulupirira Yehova.+